Jose77
Hi, please do not impersonate other people (Request for adminship). Lycaon 16:49, 8 May 2007 (UTC)
- Ok. Sorry. --Jose77 05:19, 9 May 2007 (UTC)
Timakonda kukhala ndi anthu atsopano omwe akuthandizira ku Wikipedia. Chonde musazengereze kufunsa mafunso kwa ogwiritsa ntchito ena othandiza. Chonde musati muyike mafayilo ku Wikipedia pokhapokha pali chifukwa chapadera chochitira; ntchito pa Wikimedia Commons m'malo mwake. Tikukhulupirira kuti mudzasangalala ndi nthawi imene mumakhala pano! Mukhoza kulemba mauthenga anu~~~~. |
Lycaon 08:21, 9 May 2007 (UTC)
Translation
SinthaniHi I will try Thx Ineyo
Translation
SinthaniKulandila Mzumi Woyera, kumene kumaoneka ndi kulankhula malilime, ndi kumene kumatsimikiza kuti tili ndi mbali ku ufumu wa kumwamba.
Kubatizidwa mmadzi ndi chizindikilo cha kukhululukidwa ku machimo komanso kubadwanso mwa tsopano. Kubatizidwa kotele kumayenera kuchitika pa malo amene pamapezeka madzi a chilengedwe monga pa mtsinje, pa nyanja kapenanso kasupe. Mbatizi, amene analandila kale ubatizo wa madzi ndi wa Mzimu Woyera, ndi amene amabatiza anthu m'zina la Yesu Khristu. Aliyense wobatizidwa amayenera kumizidwiratu mmadzi atawerama mutu ndikuyang'ana nkhope yake pansi.
Dongosolo lotsuka mapazi a anthu limamulola munthu kukhala ndi mbali kwa Yesu Khristu. Limakumbutsanso kuti munthu ayenera kukhala ndi chikondi, chiyero, kudzichepetsa, kukhululuka komanso kugwira ntchito ya Mulungi. Aliyense amene anabatizidwa amayeneranso kutsukidwa mapazi ake mu dzina la Yesu Khiristu. Anthu amathanso kuloledwa kutsukana mapazi.
Mgonero ndi dongosolo lokumbukira imfa ya Ambuye Yesu. Umatilora kuti tikhale ndi mbali pa imfa yake kuti tidzakhale ndi moyo wosatha ndi kudzutsidwa pa tsiku lomaliza. Dongosoloti limachitika pa nthawi ina iliyonse pafupi pafupi ndipo amagwiritsa ntchito mkate opanda chofufumitsa komanso madzi ochokera ku ma grapes okha basi.
Chichewa Wikipedia Interface
SinthaniMain Page = ? Tsamba lalikulu
Community portal = ? Tsamba la anthu wonse
Current events = ? Zomwe zikuchitika padakali pano
Recent changes = ? Kusintha kumene kwachitika posachedwa
Random page = ? Tsamba losankhidwa mopanda dongosolo
Help = ? Chithandizo
Donations = ? Tsamba lopelekelapo chithandizo cha makobili
Navigation = ? M'mene mungapezere zomwe mukufuna
Search = ? Fufuzani
Go = ? Pitani
Toolbox = ? Zida
What links here = ? Masamba olumikizana ndi tsambali
Related changes = ? Kusintha kofanana ndi tsamba lino
Upload file = ? Kulowetsa zomwe munalemba kale
Special pages = ? Masamba apadera
Printable version = ? Tsamba loti mungathe kupulinta
Permanent link = ? Kulumikiza kosachotseka
Cite this article = ? Gwiritsani ntchito tsambali pa malo ena
In other languages = ? Mu zilankhulo zina
Article = ? Tsamba
Discussion = ? Zokambirana
talk = > ZOyankhula
Edit = ? Kusintha tsamba
History = ? Mbiri ya tsamba
Delete = ? Fufutani tsamba
Protect = ? Tetezani tsamba
Log in = ? Lowani
Create Account = ? Tsegulani akaunti
Create an account = ? Tsegulani akaunti
Create article = Lembani tsamba
Not logged in = ? Simunalowe
Log out = ? Tulukani
Move = ? Samutsani
Move page = ? Samutsani tsamba
Move this page = ? Samutsani tsambali
moved to = Linasamukira ku
$1 moved to $2 = $1 linasamukira ku $2
Reason = Chifukwa
Watch = ? Penyani tsambali
My Watchlist = ? Ndondomeko ya masamba amene ndikuwapenyetsetsa
My talk = ? Ndondomeko yanga yoyankhula ndi anthu ena
My preferences = ? Chisankho changa cha mmene masamba aziwonekera
My contributions = ? Zolemba zanga m'bukhuli
Summary = ? Mwa chidule
This is a minor edit = ? Kusintha uku ndi kwa pang'ono
Watch this page = ? Wonetsetsani tsamba ili
Save page = ? Sungani tsamba m'bukhuli
Show preview = ? Onetsani m'mene tsamba lasinthila
Show changes = ? Onetsani zimene zasintha pa tsambali
Cancel = ? Siyani, musasinthenso
Editing Help = ? Chithandizo chosinthila bukhuli
User page = ? Tsamba la iwe mwini
Username = ? Dzina logwiritsa ntchito
Password = ? Liu la chitetezo
Re-type password = ? Lembaninso liu la chitetezo
E-mail = ? Kalata ya pa kompyuta
System messages = ? Mauthenga ochokera mmakina
System messages = ?
Remember my login on this computer = ? Mukumbukire dzina langa pa makinawa
User:Contributions = ? Wogwiritsa ntchito:zosintha
Login required to edit = ? Kulowa kdi kofunika kuti tsambali lisinthidwe
View source = ? Kuona kumene tsambali lachokera
new messages = ? Mauthenga atsopano
You have new messages on $1 = ? Muli ndi mauthenga atsopano
== Welcome, $1! == Your account has been created. Don't forget to change your Wikipedia preferences. = ?
==Mwalandiridwa, $1!== Akaunti yanu ya Wikipedia tsopano yatsegulidwa. Chonde musayiwale kusintha m'mene mukufuna kuti masamba anu adziwonekera.
January Januale
February Febuluale
March Malichi
April Epulo
May Meyi
June Juni
July Julaye
August Ogasiti
September Sepitembala
October Okotobala
November Novembala
December Disembala
Sunday Lasabata
Monday Lolemba
Tuesday Lachiwiri
Wednesday Lachitatu
Thursday Lachinayi
Friday Lachisanu
Saturday Loweruka
Disclaimers Zomwe bukuli silidzakhala nazo ndi mulandu
Privacy Policy Malamulo okhudza chinsinsi cha zolembedwa m'bukhuli
About Wikipedia Zokhudza Wikipedia
Adminship
SinthaniFor now I'd rather just translate the articles, but thanks for your nomination. By the way, I'm a she, not a he :-D Ineyo 08:48, 17 May 2007 (UTC)
Your account will be renamed
SinthaniHello,
The developer team at Wikimedia is making some changes to how accounts work, as part of our on-going efforts to provide new and better tools for our users like cross-wiki notifications. These changes will mean you have the same account name everywhere. This will let us give you new features that will help you edit and discuss better, and allow more flexible user permissions for tools. One of the side-effects of this is that user accounts will now have to be unique across all 900 Wikimedia wikis. See the announcement for more information.
Unfortunately, your account clashes with another account also called Jose77. To make sure that both of you can use all Wikimedia projects in future, we have reserved the name Jose77~nywiki that only you will have. If you like it, you don't have to do anything. If you do not like it, you can pick out a different name.
Your account will still work as before, and you will be credited for all your edits made so far, but you will have to use the new account name when you log in.
Sorry for the inconvenience.
Yours,
Keegan Peterzell
Community Liaison, Wikimedia Foundation
04:22, 18 March 2015 (UTC)