Kapichira
Ili ndi dzina la Malo opangilapo mphamvu ya Magesti kudzera njira ya madzi (Hydro electric Power Plant) omwe amapzeka ku madzulo kwa dziko la Malawi, mu boma la Chikwawa. Malo a Kapichira amatulutsa mphamvu ya magetsi yokawana 66 Mega Watts. Kuchokera mu mzinda wa Blantyre, ulendo wopita umatenga ma ola osachepera atatu (3 Hours), koma ntawi iyi imatengela ndi liwilo lomwe inu mungayende.