Zimbabwe ndi limodzi mwa maiko a kumwera kwa Afrika ndipo dzikoli ndi lomwe kale linkalamuliridwa muchisamunda cha angerezi pomwe akalitchula kuti Rhodesia. Nsogoleri wadzikoli pakali pano ndi is VACANT amene anayamba kulamulira dzikoli pamene linalanda ulamuliro kuchokera kwa angerezi m'chaka cha 1980.

Potsatira zokambirana zothetsa mapokoso ndi chipolowe chomwe chinabuka pambuyo pamasankho apa 21 Marichi, 2008 a Morgan Tshangirai omwe ndi m'tsogoleri wa chipani cha Movement for Democratic Change anakhala Nduna yaikulu ya boma. New leader of Zimbabwe 24 November 2017 is Emmerson Mnangagwa.


Zimbabwe