Wolembedwa ndi Yohane
(Redirected from Yohane)
- Pachiyambi pa zonse Iye amene amatchedwa dzina loti Mawu, analipo kale. Anali kwa Mulungu, Edipo anali Mulungu.
- Anali kwa Mulungu chiyambire.
- Mulungu analenga zonse ndi lye, Edipo popanda Iye sanalenge kanthu kalikonse.
- Mwa Iyeyo munali moyo, Edipo moyowo unalikuŵalira anthu.
- Kuŵalako kulikuunikabe mandita, Edipo nyima unalephera kugonjetsa kuŵalako.
- Mulungu anatema munthu wina, dzina lake Yohanne.
- Iye anabwera kudzachitira umboni wakewo.
- Si kuti iyeyo anali kuŵalako ayi, koma anangobwera kudzachitira umboni kuŵalako.
- Kuŵala kwenikweni, kounikira anthu onse, kunalikudza pansi pano.
- Mawuwo anali n’dzino lapansi, Edipo Mulungu analenga dziko lapansi ndi Iye, komabe anthu a pansi pano sanamzindikire.