Wikipedia mu Chichewa
ChiChewa-chinenero cha Wikipedia
(Redirected from Wikipedia ya Chewa)
Chi-Chewa Wikipedia ndi tsamba la Wikipedia mu chinenelo cha Chichewa (Chinyanja). Tsambali limayendtsedwa ndi Wikimedia Foundation ndipo idayambika pa 9 May 2007. Lili ndi mutu yayikulu yoposa 1,076 pofika lero.

Ogwiritsa ntchito ndi olemba
SinthaniChiwerengero cha ma akaunti osuta | Chiwerengero cha nkhani | Chiwerengero cha mafayela | Chiwerengero cha olamulira |
---|---|---|---|
11792[1] | 1076[1] | 0[1] | 2[1] |
References
Sinthani- ↑ 1.0 1.1 1.2 1.3 "Statistics", Wikipedia, retrieved 2018-10-20