Mulanje ndi mzinda ku dziko la Malaŵi. Ku Mulanje ndi dera limene kumapezeka phiri lalikulu mu malawi yonse. Phirili ndi lachitatu kukula mu africa yonse.[1]