Mic Burner

Mic Burner, ndi wolemba na ku yimba nyimbo mu Zambia.

Michael Mandona (wobadwa pa May 31, 1990)[1] wodziwika bwino monga Mic Burner, ndi wolemba na ku yimba nyimbo mu Zambia.[2][3] Ye amadziwika bwino chifukwa cha nyimbo Thought of You ndi bajeti ya US $ 50,000 ndipo adawombera ku South Africa ndi Namibia. Atabadwira ku Ndola adapita ku sukulu ya St. Andrews High School koma adaphunzira maphunziro ake ku Grade 12 ku Kamwala High School mu Lusaka.[4]

Zogwirizana zakunja

Sinthani
  1. "MIC BURNER BIO". MIC BURNER (in English). Retrieved 2018-08-21.
  2. "Zed Top 10: Mic Burner brings the Fire". Zambezi Magic - Channel 160 - Zed Top 10: Mic Burner brings the Fire. (in English). Retrieved 2018-08-17.
  3. "Behind The Music: Mic Burner's "Fuss"". Zambezi Magic - Channel 160 - Behind The Music: Mic Burner's "Fuss" (in English). Retrieved 2018-08-17.
  4. "Mic Burner to premiere $50,000 music video – Zambia Daily Mail". www.daily-mail.co.zm (in English). Retrieved 2018-08-17.