Sulaiman Kalimu Mwana wa number 3 mubanja la Ana 6 Ku salima Malawi ku lifidzi. school Ali form 2.chipembedzo chake ndi chisila. Ali ndi mayina angapo. Loyamba Sulaiman (birth name). Jovanie mw (Nickname). Ishmael (at school)Amavera nyimbo ZA Malinga Mafia. Amadana ndi nyimbo za Mady p (don gogo) Amasapota BEFOWARD WANDERERS (manoma) Kunja amasapota team ya MANCHESTER UNITED PLAYER YEMWE AMAMUKONDA NDI CHRITIANAL RONALDO. AMAKONDA KUSEWERA GAME YA DREAM LEAGUE nzake wa pantima ndi BONIFACE KILEMBE Adaimako ndi malinga nyimbo yotchedwa #RIGHT #STARS muchaka cha 2019 Nyimbo ina adaimba ndi B WILLZ (Boniface kilimbe) Nyimbo yotchedwa Mu GHETTO

SULAIMAN ABDUL KAREEM Adabadwa pa 27th may 2002 Kwa kutsanja