Interface Adminstrator
Interface Adminstrator ndi woyang'anila Wikipediya odalilika kwambili amene amatanthauzila zolemba za Wikipediya kukhala mu chiyankhulo chofunikila komanso amasintha ndi kupanga masamba ofunikila kwambili otchedwa CSS amene amathandiza kuti Wikipediya iziyenda bwino. Masamba otchedwa CSS ndi masamba apamwamba kwambili amene akasinthidwa pang'ono mwangozi, Wikipediya yose imasiya kugwila ntchito pompo mpaka atakonzedwa.
Choncho udindowu umafuna munthu amene akudziwa bwino mmene developing, encoding (kupanga tsamba) ndi zina zimayendela. Chifukwa kusadziwa bwino, Wikipediya yonse imathe pompo.
Ntchito za Interface Adminstrator
- Kupanga style ya matsamba
- Kulemba masamba a CSS amene Wikipedia imadalila.
- Kuteteza matsamba
- Kubloka agwilitsi opanga zawo zawo.
- Kulemba matsamba otchedwa Jason.
- Kutanthauzila Main Page Interface.
- Kubisa mbili ya masamba.
- Kulemba masamba a munthu ogwilista ntchito.