Baibulo

Baibulo ndi buku lopatulika lomwe limakhulupiliwa kuti linapatsidwa kwa anthu kuchokera kwa Mulungu. Ilo lagawidwa muzigawo ziwiri- malemba a Chiheberi ndi malemba a Chigriki. Mabukhu amene amagwiritsidwa ntchito ku Chiyuda amatchedwa Tanaka kapena Baibulo la Chiyunda. Mabukhu amene amagwiritsidwa ntchito mu Chikhristu amatcheda Bukhu Loyera, Mau a Mulungu kapena Baibulo la chi Khristu. Chikhristu chimatenga ma bukhu ena a Baibulo la Chiyuda ku Chipangano cha kale, ngakhale ma bukhu awa amasiyana pa dongosolo lake ndipo ma baibulo ena ali ndi mabukhu owonjezera. baibulo la Chikhristu lili ndi mbali ina ya chiwiri yotchedwa Chipangano cha Tsopano.

Baibulo

Mabukhu a BaibuloEdit

Ma bukhu a baibulo amayalidwa mofanana mu zitanthauziro zosiyana siyana. Baibulo la Chikhristu linagawidwa mbali ziwili: Chipangano cha Kale ndi Chipangano cha Tsopano.

Chipangano cha KaleEdit

GenesisEdit

EkesodoEdit

20

NumeriEdit

DeuteronomoEdit

YoswaEdit

OweruzaEdit

RuteEdit

1 SamueliEdit

2 SamueliEdit

1 MafumuEdit

2 MafumuEdit

1 MbiriEdit

2 MbiriEdit

EzaraEdit

NehemiyaEdit

EstereEdit

YobuEdit

MasalimoEdit

MiyamboEdit

MlalikiEdit

Nyimbo ya SolomoEdit

YesayaEdit

YeremiyaEdit

MaliroEdit

EzekieliEdit

DanieliEdit

HoseyaEdit

YoweriEdit

ObadiyaEdit

YonaEdit

MikaEdit

NahamuEdit

HabakukuEdit

ZefaniyaEdit

HagaiEdit

ZekariyaEdit

MalakiEdit

Chipangano cha TsopanoEdit

MateyuEdit

MalikoEdit

LukaEdit

YohaneEdit

Machitidwe a AtumwiEdit

AromaEdit

1 AkorintoEdit

2 AkorintoEdit

AfilipiEdit

AkoloseEdit

1 AtesalonikaEdit

2 AtesalonikaEdit

1 TimoteyoEdit

2 TimoteyoEdit

TitoEdit

AhebriEdit

YakoboEdit

1 PetroEdit

2 PetroEdit

1 YohaneEdit

2 YohaneEdit

3 YohaneEdit

YudaEdit

ChibvumbulutsoEdit