Open main menu

Wikipedia β

Alliance for Democracy

Chipani cha Alliance for Democracy ndi chipani cha ndale ku Malaŵi chimene chili ndi mphamvu kwambiri kumpoto kwa dzikoli. Anayambitsa chipanichi ndi a Chakufwa Chihana amene anatsogolera chipanichi mpaka pa nthawi yomwe anamwalira mu 2006. Pa chisankho cha 2004, chipanichi chinapeza mipando 6 ya mipando 94 yomwe inalipo wa ma Member of Parliament, ndipo pa chisankho cha 2004 chimene anapampana a Bingu wa Muntharika chinapeza mpando umodzi wokha.

Atamwalira a Chihana, atsogoleri a chipanichi akhala akukanganira utsogoleri.