Dedza ndi boma lina la dziko la Malawi.

Dedza
Golomoti escarpment ku Dedza.

Bomali liri pa malire ndi maboma a Ntcheu, Lilongwe, Salima, Mangochi, Balaka Komanso Mozambique. Anthu ambiri amachita malonda awo ngakhalenso maukwati ndi anthu a ku Mozambique.

Link Sinthani

  Dedza