Chinenelo cha dziko

Chinenelo cha dzika ndi chilankhulo chomwe anthu a dziko amalankhula. Chinenelochi chimasankhidwa ndi boma la dziko.